Uchi Woyee , livre ebook

icon

33

pages

icon

English

icon

Ebooks

2024

Écrit par

Publié par

Lire un extrait
Lire un extrait

Obtenez un accès à la bibliothèque pour le consulter en ligne En savoir plus

Découvre YouScribe et accède à tout notre catalogue !

Je m'inscris

Découvre YouScribe et accède à tout notre catalogue !

Je m'inscris
icon

33

pages

icon

English

icon

Ebooks

2024

Lire un extrait
Lire un extrait

Obtenez un accès à la bibliothèque pour le consulter en ligne En savoir plus

Atazizwa ndi ubwino wosiyanasiyana wa uchi, mwana anafuna kudziwa momwe njuchi zimapangira uchi. Amalume ake akufotokoza bwino lomwe za m'gwirizano wa njuchi ndi ukatswiri wakapangidwe ka uchi. Akufotokozanso za ntchito zina za uchi monga kuthandiza pa matenda ena.
After tasting the sweetness of honey, Chifundo is interested to know the honey -making process. Her uncle takes her through the process from nectar collection to the hive and all the intricate operations of the bees up to placement of ripe honey in wax cells. The exciting behaviour of bees is unveiled. The uncle also talks of honey harvesting and health benefits.
Voir icon arrow

Publié par

Date de parution

08 août 2024

EAN13

9789996083365

Langue

English

Poids de l'ouvrage

36 Mo

UCHI WOYEE!
1
Wofalisa:
Horace Publications Private Bag 140, Blantyre, Malawi.
ISBN978-99960-83-36-5
Woyala bukhu: Thom Mvula
2
Chifundo anakonda uchi womwe mayi ake anabweretsa. Atathira m’tiyi, iye ananyambitira wotsalira womwe unali pachala chake. Chifundo anafuna kudziwa zambiri za kapangidwe ka uchi.
5
Voir icon more
Alternate Text